Psalms 94:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mumampumitsa pa nthaŵi yamavuto, mpaka woipa ataloŵa m'dzenje.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti mumpumitse masiku oipa; kufikira atakumbira woipa mbuna.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mumamupumitsa pa nthawi ya mavuto, mpaka woyipa atakumbiridwa dzenje.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti mumpumitse masiku oipa; Kufikira atakumbira woipa mbuna.