Psalms 94:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndani amalimba mtima kuti andimenyere nkhondo ndi anthu oipa? Ndani amaimira mbali yanga, kuti alimbane ndi anthu ochita zoipa?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzandiukira ndani kutsutsana nao ochita zoipa? Adzandilimbikira ndani kutsutsana nao ochita zopanda pake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndani adzadzuka chifukwa cha ine kulimbana ndi anthu oyipa? Ndani adzayimirira mʼmalo mwanga kulimbana ndi anthu ochita zoyipa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzandiukira ndani kutsutsana nao ocita zoipa? Adzandilimbikira ndani kutsutsana nao ocita zopanda pace?