Psalms 94:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akadapanda kundithandiza, bwenzi posachedwa nditapita ku dziko lazii.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akadapanda kukhala thandizo langa Yehova, moyo wanga ukadakhala kuli chete.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akanapanda kundithandiza, bwenzi nditakakhala msanga ku malo achete a imfa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akadapanda kukhala thandizo langa Yehova, Moyo wanga ukadakhala kuli cete.