Psalms 94:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene nkhaŵa zikundichulukira, Inu mumasangalatsa mtima wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pondichulukira zolingalira zanga m'kati mwanga, zotonthoza zanu zikondweretsa moyo wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene nkhawa inakula mʼkati mwanga, chitonthozo chanu chinabweretsa chimwemwe mʼmoyo mwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pondicurukira zolingalira zanga m'kati mwanga, Zotonthoza zanu zikondweretsa moyo wanga.