Psalms 94:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi angathe kugwirizana nanu olamulira oipa, amene amapotoza malamulo anu olungama?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi uyenera kuyanjana ndi Inu mpando wachifumu wa kusakaza, wakupanga chovuta chikhale lamulo?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi mpando waufumu woyipa ungathe kugwirizana nanu umene umabweretsa masautso chifukwa cha malamulo ake?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi uyenera kuyanjana ndi Inu mpando wacifumu wa kusakaza, Wakupanga cobvuta cikhale lamulo?