Psalms 94:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amagwirizana kuti aononge anthu osalakwa, nagamula kuti opanda mlandu aphedwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Asonkhana pamodzi pa moyo wa wolungama, namtsutsa wa mwazi wosachimwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amasonkhana pamodzi kulimbana ndi wolungama ndi kugamula kuti wosalakwa aphedwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Asonkhana pamodzi pa moyo wa wolungama, Namtsutsa wa mwazi wosacimwa.