Psalms 94:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzaŵalanga chifukwa cha machimo ao, adzaŵaononga chifukwa cha kuipa kwao, zoonadi, Chauta, Mulungu wathu, ndiye amene adzaŵafafanize.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anawabwezera zopanda pake zao, nadzawaononga m'choipa chao; Yehova Mulungu wathu adzawaononga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye adzawabwezera chifukwa cha machimo awo ndi kuwawononga chifukwa cha kuyipa kwawo; Yehova Mulungu wathu adzawawononga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anawabwezera zopanda pace zao, Nadzawaononga m'coipa cao; Yehova Mulungu wathu adzawaononga.