Psalms 94:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, kodi anthu oipa adzadzitamabe mpaka liti?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Oipa adzatumpha ndi chimwemwe kufikira liti, Yehova? Oipa adzatero kufikira liti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi mpaka liti anthu oyipa Inu Yehova, mpaka liti anthu oyipa adzalumpha ndi chimwemwe?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Oipa adzatumpha ndi cimwemwe kufikira liti, Yehova? Oipa adzatero kufikira liti?