Psalms 94:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amatswanya anthu anu, Inu Chauta, amazunza anthu anu osankhidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Aphwanya anthu anu, Yehova, nazunza cholandira chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amaphwanya anthu anu, Inu Yehova; amapondereza cholowa chanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aphwanya anthu anu, Yehova, Nazunza colandira canu.