Psalms 94:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amapha akazi amasiye ndi alendo okhala nawo m'dziko mwao, amaphanso ana amasiye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amapha wamasiye ndi mlendo, nawapha ana amasiye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amaphanso amayi a masiye ndi alendo okhala nawo mʼdziko; amapha ana amasiye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amapha wamasiye ndi mlendo, Nawapha ana amasiye.