Psalms 94:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka amati, “Chauta sakuwona, Mulungu wa Yakobe sakuzidziŵa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo amati, Yehova sachipenya, ndi Mulungu wa Yakobo sachisamalira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amati, “Yehova sakuona; Mulungu wa Yakobo salabadirako.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo amati, Yehova sacipenya, Ndi Mulungu wa Yakobo sacisamalira.