Psalms 94:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mvetsani anthu opusa kwambirinu. Zitsiru inu, mudzakhala ndi nzeru liti?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zindikirani, opulukira inu mwa anthu; ndipo opusa inu, mudzachita mwanzeru liti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Samalani, inu anthu opanda nzeru pakati pa anthu; zitsiru inu, kodi mudzakhala liti anzeru?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zindikirani, opulukira inu mwa anthu; Ndipo opusa inu, mudzacita mwanzeru liti?