Psalms 95:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho ndidakwiya nkulumbira kuti anthuwo sadzaloŵa ku malo anga ampumulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake ndinalumbira mu mkwiyo wanga, ngati adzalowa mpumulo wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho ndili chikwiyire, ndinalumbira kuti, “Iwowa sadzalowa ku malo anga a mpumulo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace ndinalumbira mu mkwiyo wanga, Ngati adzalowa mpumulo wanga.