Psalms 95:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maziko ozama a dziko lapansi ali m'manja mwake. Mapiri aatali omwe ngakenso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Malo ozama a dziko lapansi ali m'dzanja lake; chuma cha m'mapiri chomwe ndi chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmanja mwake muli maziko ozama a dziko lapansi, ndipo msonga za mapiri ndi zake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Malo ozama a dziko lapansi ali m'dzanja lace; Cuma ca m'mapiri comwe ndi cace.