Psalms 95:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nyanja ndi yake, popeza kuti ndiye adailenga. Mtunda ndi wakenso, popeza kuti ndiye adaupanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyanja ndi yake, anailenga; ndipo manja ake anaumba dziko louma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyanja ndi yake, pakuti anayilenga ndi Iye, ndipo manja ake anawumba mtunda wowuma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nyanja ndi yace, anailenga; Ndipo manja ace anaumba dziko louma.