Psalms 95:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti ndiye Mulungu wathu, ndipo ife ndife anthu a pa busa lake, ndife nkhosa zodyera m'manja mwake. Lero mukadamverako mau ake!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Iye ndiye Mulungu wathu, ndipo ife ndife anthu a pabusa pake, ndi nkhosa za m'dzanja mwake. Lero, mukamva mau ake!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti Iye ndiye Mulungu wathu ndipo ife ndife anthu a pabusa pake, ndi nkhosa za mʼdzanja lake. Lero ngati inu mumva mawu ake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Iye ndiye Mulungu wathu, Ndipo ife ndife anthu a pabusa pace, ndi nkhosa za m'dzanja mwace. Lero, mukamva mau acel