Psalms 95:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pamene makolo anu adandiputa mondiyesa ngakhale anali ataona ntchito zanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene makolo anu anandisuntha, anandiyesa, anapenyanso chochita Ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumene makolo anu anandiyesa ndi kundiputa, ngakhale anaona zimene Ine ndinazichita.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene makolo anu anandisuntha, Anandiyesa, anapenyanso cocita Ine.