Psalms 96:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Uzani mitundu ya anthu kuti, “Chauta ndiye Mfumu. Dziko lonse lidakhazikitsidwa molimba, silidzagwedezeka konse. Adzaweruza mitundu yonse ya anthu mwachilungamo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nenani mwa amitundu, Yehova achita ufumu; dziko lokhalamo anthu lomwe likhazikika kuti silingagwedezeke; adzaweruza mitundu ya anthu molunjika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nenani pakati pa mitundu ya anthu, “Yehova akulamulira.” Dziko lonse lakhazikika molimba, silingasunthidwe; Iye adzaweruza mitundu ya anthu molungama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nenani mwa amitundu, Yehova acita ufumu; Dziko lokhalamo anthu lomwe likhazikika kuti silingagwedezeke; Adzaweruza mitundu ya anthu molunjika.