Psalms 96:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zakumwamba zisangalale, zapansi pano zikondwere, nyanja ikokome pamodzi ndi zonse zam'menemo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumwamba kukondwere nilisekerere dziko lapansi; nyanja ibume mwa kudzala kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mayiko akumwamba asangalale, dziko lapansi likondwere; nyanja ikokome, ndi zonse zili mʼmenemo;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumwamba kukondwere nilisekerere dziko lapansi; Nyanja ibume mwa kudzala kwace: