Psalms 96:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pamaso pa Chauta, pamene zabwera kudzalamulira dziko lapansi. Adzalamulira dziko lonse mwachilungamo, adzalamulira anthu a mitundu yonse moona.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamaso pa Yehova, pakuti akudza; pakuti akudza kudzaweruza dziko lapansi Adzaweruza dziko lokhalamo anthu ndi chilungamo, ndi mitundu ya anthu ndi choonadi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
idzayimba pamaso pa Yehova, pakuti Iye akubwera kudzaweruza dziko lapansi; adzaweruza dziko lonse mwachilungamo ndi mitundu ya anthu onse mʼchoonadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamaso pa Yehova, pakuti akudza; Pakuti akudza kudzaweruza dziko lapansi: Adzaweruza dziko lokhalamo anthu ndi cilungamo, Ndi mitundu ya anthu ndi coonadi.