Psalms 96:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja milungu yonse ya mitundu ina ya anthu ndi mafano chabe. Koma Chauta ndiye adalenga zakumwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti milungu yonse ya mitundu ya anthu ndiyo mafano, koma Yehova analenga zakumwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi mafano, koma Yehova analenga mayiko akumwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti milungu yonse ya mitundu ya anthu ndiyo mafano: Koma Yehova analenga zakumwamba.