Psalms 96:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tamandani, inu anthu a mitundu yonse, vomerezani kuti ulemerero ndi mphamvu, zonse nzake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mpatseni Yehova, inu, mafuko a mitundu ya anthu, mpatseni Yehova ulemerero ndi mphamvu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Perekani kwa Yehova, inu mabanja a anthu a mitundu ina, perekani kwa Yehova ulemerero ndi mphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mpatseni Yehova, inu, mafuko a mitundu ya anthu, Mpatseni Yehova ulemerero ndi mphamvu,