Psalms 96:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pembedzani Chauta waulemerero ndi woyera, njenjemerani pamaso pake, inu anthu onse a pa dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Gwadirani Yehova moyera ndi mokometsetsa, njenjemerani pamaso pake, inu dziko lonse lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lambirani Yehova mu ulemerero wa chiyero chake; njenjemerani pamaso pake, dziko lonse lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Gwadirani Yehova moyera ndi mokometsetsa: Njenjemerani pamaso pace, inu dziko lonse lapansi.