Psalms 97:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta ndiye Mfumu, anthu a pa dziko lapansi akondwere, anthu onse a m'mbali mwa nyanja asangalale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova achita ufumu; dziko lapansi likondwere; zisumbu zambiri zikondwerere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akulamulira, dziko lapansi lisangalale; magombe akutali akondwere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova acita ufumu; dziko lapansi likondwere; Zisumbu zambiri zikondwerere.