Psalms 97:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mitambo ndi mdima waukulu zamzinga Chauta. Amalamulira molungama, mu ufumu wake mulibe tsankho.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pomzinga pali mitambo ndi mdima; chilungamo ndi chiweruzo ndizo zolimbitsa mpando wachifumu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mitambo ndi mdima waukulu zamuzungulira; chilungamo ndi kuweruza molungama ndiwo maziko a mpando wake waufumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pomzinga pali mitambo ndi mdima; Cilungamo ndi ciweruzo ndizo zolimbitsa mpando wacifumu wace.