Psalms 97:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a ku Ziyoni akumva, ndipo akusangalala, midzi ya ku Yuda nayonso ikukondwera chifukwa cha kaweruzidwe kanu, Inu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ziyoni anamva nakondwera, nasekerera ana akazi a Yuda; chifukwa cha maweruzo anu, Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ziyoni akumva ndipo akukondwera, midzi ya Yuda ikusangalala chifukwa cha maweruzo anu Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ziyoni anamva nakondwera, Nasekerera ana akazi a Yuda; Cifukwa ca maweruzo anu, Yehova.