Psalms 97:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti Inu Chauta ndinu Wopambanazonse, wolamulira dziko lonse lapansi. Ndinu amphamvu kupambana milungu yonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Inu, Yehova, ndinu Wam'mwambamwamba pa dziko lonse lapansi, ndinu wokwezeka kwakukulu pamwamba pa milungu yonse ina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Inu Yehova ndi Wammwambamwamba pa dziko lonse lapansi; ndinu wokwezeka kupambana milungu yonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Inu, Yehova, ndinu Wam'mwambamwamba pa dziko lonse lapansi, Ndinu wokwezeka kwakukuru pamwamba pa milungu yonse yina.