Psalms 98:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Imbirani Chauta nyimbo yatsopano, popeza kuti wachita zodabwitsa. Dzanja lake lamanja ndi mkono wake woyera zampambanitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Salimo. Muimbireni Yehova nyimbo yatsopano; popeza anachita zodabwitsa: Dzanja lake lamanja, mkono wake woyera, zinamchitira chipulumutso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salimo. Imbirani Yehova nyimbo yatsopano, pakuti Iyeyo wachita zinthu zodabwitsa; dzanja lake lamanja ndi mkono wake woyera zamuchitira chipulumutso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Myimbireni Yehova nyimbo yatsopano; Popeza anacita zodabwiza: Dzanja lace lamanja, mkono wace woyera, zinamcitira cipulumutso,