Psalms 98:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta waonetsa kuti Iye wapambana pa nkhondo, waulula pamaso pa anthu a mitundu yonse kuti Iye ndi wolungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova anawadziwitsira chipulumutso chake; anaonetsera chilungamo chake pamaso pa amitundu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova waonetsa chipulumutso chake ndipo waulula chilungamo chake kwa anthu a mitundu ina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova anawadziwitsira cipulumutso cace; Anaonetsera cilungamo cace pamaso pa amitundu.