Psalms 98:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Fuulirani Chauta ndi chimwemwe, inu dziko lonse lapansi. Muimbireni mokondwa nyimbo zotamanda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Fuulirani kwa Yehova, inu, dziko lonse lapansi; kuwitsani ndi kufuulira mokondwera; inde, imbirani zomlemekeza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Fuwulani mwachimwemwe kwa Yehova, dziko lonse lapansi, muyimbireni nyimbo mofuwula ndi mokondwera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pfuulirani kwa Yehova, inu, dziko lonse lapansi; Kuwitsani ndi kupfuulira mokondwera; inde, yimbirani zomlemekeza.