Psalms 98:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Imbirani Chauta Mfumu, imbani molimbika ndi malipenga ndi mbetete.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Fuulani pamaso pa Mfumu Yehova, ndi mbetete ndi liu la lipenga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi malipenga ndi kuliza kwa nyanga ya nkhosa yayimuna fuwulani mwachimwemwe pamaso pa Yehova Mfumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pfuulani pamaso pa Mfumu Yehova, Ndi mbetete ndi liu la lipenga,