Psalms 98:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nyanja ikokome pamodzi ndi zonse zam'menemo, dziko lifuule pamodzi ndi anthu onse am'menemo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyanja ifuule ndi kudzala kwake; dziko lokhalamo anthu ndi iwo okhalamo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyanja ikokome pamodzi ndi zonse zili mʼmenemo, dziko lonse ndi onse amene amakhala mʼmenemo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nyanja Ipfuule ndi kudzala kwace; Dziko lokhalamo anthu ndi iwo okhalamo;