Psalms 98:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pamene Chauta akufika, popeza kuti akubwera kudzaweruza dziko lapansi. Adzaweruza dziko lonse mwachilungamo, adzaweruza mitundu yonse mosakondera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamaso pa Yehova, popeza akudza kudzaweruza dziko lapansi; adzaweruza dziko lokhalamo anthu ndi chilungamo, ndipo mitundu ya anthu molunjika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
izo ziyimbe pamaso pa Yehova, pakuti Iye akubwera kudzaweruza dziko lapansi. Adzaweruza dziko lonse mwachilungamo, ndi mitundu ya anthu mosakondera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamaso pa Yehova, popeza akudza kudzaweruza dziko lapansi; Adzaweruza dziko lokhalamo anthu ndi cilungamo, Ndi mitundu ya anthu molunjika,