Psalms 99:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta ndiye mfumu, mitundu ya anthu injenjemere. Wakhala pa akerubi ngati pa mpando wake wachifumu. Dziko lapansi ligwedezeke!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova ndiye mfumu; mitundu ya anthu injenjemere; Iye akhala pakati pa akerubi; dziko lapansi ligwedezeke.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akulamulira, mitundu ya anthu injenjemere; Iye wakhala pa mpando wake waufumu, pakati pa akerubi, dziko lapansi ligwedezeke.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova ndiye mfumu; mitundu ya anthu injenjemere; Iye akhala pakati pa akerubi; dziko lapansi ligwedezeke.