Psalms 99:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onse atamande dzina lake lalikulu ndi loopsa! Iye ndi woyera!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Alemekeze dzina lanu lalikulu ndi loopsa. Ili ndilo loyera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu atamande dzina lanu lalikulu ndi loopsa kwambiri, Iye ndi woyera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Alemekeze dzina lanu lalikuru ndi loopsa; Ili ndilo loyera.