Psalms 99:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankalankhula nawo mu mtambo woima kuti njo. Iwo ankasunga mapangano ndi malangizo amene Iye adaŵapatsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye analankhula nao mu mtambo woti njo: Iwo anasunga mboni zake ndi malembawa anawapatsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anayankhula nawo kuchokera mʼchipilala cha mtambo; iwo anasunga malamulo ake ndi zophunzitsa zomwe anawapatsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye analankhula nao mumtambo woti njo: Iwo anasunga mboni zace ndi malembawa anawapatsa,