Psalms 99:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, Mulungu wathu, munkaŵayankha, munali Mulungu woŵakhululukira, komabe wolanga ntchito zao zoipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munawayankha, Yehova Mulungu wathu: munawakhalira Mulungu wakuwakhululukira, mungakhale munabwezera chilango pa zochita zao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Yehova Mulungu wathu, munawayankha iwo; Inu kwa Israeli munali Mulungu wokhululuka, ngakhale munawalanga pa zochita zawo zoyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munawayankha, Yehova Mulungu wathu: Munawakhalira Mulungu wakuwakhululukira, Mungakhale munabwezera cilango pa zocita zao.