Revelation 1:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsitsi lake linali loyera ngati thonje loyera kwambiri, ngati chipale chambee; maso ake ngati malaŵi a moto;
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsitsi la pamutu pake linali loyera ngati ubweya woyera, ngati chipale chofewa; ndi maso ake ngati lawi la moto;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsitsi lake linali loyera ngati thonje, kuyera ngati matalala, ndipo maso ake amawala ngati malawi amoto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsitsi la pamutu pace linali loyera ngati ubweya woyera, ngati cipale cofewa; ndi maso ace ngati lawi la moto;