Revelation 1:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lemba tsono zimene waziwona, ndiye kuti zimene zikuchitika tsopano ndi zimene zidzachitike bwino lino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake lemba zimene unaziona, ndi zimene zilipo, ndi zimene zidzaoneka m'tsogolomo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Chomwecho, lemba zimene waona, zimene zilipo panopa ndi zimene zidzachitike mʼtsogolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace 2 lembera zimene unaziona, ndi zimene ziripo, ndi zimene zidzaoneka m'tsogolomo;