Revelation 11:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wina aliyense akafuna kuzipweteka mbonizo, moto umatuluka kukamwa kwao nkuwononga adani aowo. Ndipo munthu aliyense wofuna kuzipweteka, adzayenera kuphedwa mwa njira yomweyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo wina akafuna kuipsa izo, moto utuluka m'kamwa mwao, nuononga adani ao; ndipo wina akafuna kuipsa izo, maphedwe ake ayenera kutero.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati wina atafuna kuzipweteka mbonizo, moto umatuluka mʼkamwa mwawo ndikuwononga adani awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo wina akafuna kuipsa izo, moto uturuka m'kamwa mwao, nuononga adani ao; ndipo wina akafuna kuipsa izo, maphedwe ace ayenera kutero.