Revelation 12:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono chinjoka chija chitaona kuti chagwetsedwa pa dziko lapansi, chidayamba kumpirikitsa mai uja amene anali atabala mwana wamwamuna.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene chinjoka chinaona kuti chinaponyedwa pansi kudziko, chinazunza mkazi amene adabala mwana wamwamuna.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene chinjokacho chinaona kuti chagwetsedwa pa dziko lapansi, chinayamba kuthamangitsa mayi uja amene anali atabala mwana wamwamunayu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene cinjoka cinaonakuticinaponyedwa pansikudziko, cinazunza mkazi amene adabala mwana wamwamuna.