Revelation 12:18 — Compare Translations

2 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chinjokacho chinakaimirira m'mbali mwa nyanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka ndinaona chinjokacho chitayima mʼmbali mwa nyanja.