Revelation 12:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maiyo anali ndi pathupi, ndipo pa nthaŵi yochira adalira nako mokuwa kupweteka kwa kubala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anali ndi pakati; ndipo afuula alimkubala, ndi kumva zowawa zakubala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mayiyo anali woyembekezera ndipo pa nthawi yake yochira analira mokuwa chifukwa cha ululu wakubala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anali ndi pakati; ndipo apfuula alimkubala, ndi kumva zowawa zakubala.