Revelation 12:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maiyo adabala mwana wamwamuna, woyenera kudzalamulira anthu a mitundu yonse ndi ndodo yachitsulo. Mwanayo adalandidwa kumanja kwa mai wake kupita naye kwa Mulungu ndi ku mpando wake wachifumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anabala mwana wamwamuna, amene adzaweruza mitundu yonse ndi ndodo yachitsulo: ndipo anakwatulidwa mwana wake amuke kwa Mulungu, ndi kumpando wachifumu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mayiyo anabereka mwana wamwamuna amene adzalamulira anthu a mitundu ina yonse ndi ndodo yachitsulo. Ndipo mwanayo analandidwa ku dzanja la mayiyo ndi kupita naye kwa Mulungu ku mpando wake waufumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anabala mwana wamwamuna, amene adzaweruza mitundu yonse ndi ndodo yacitsulo: ndipo anakwatulidwa mwana wace amuke kwa Mulungu, ndi ku mpando wacifumu wace.