Revelation 14:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake mngelo wina adatuluka m'Nyumba ya Mulungu Kumwamba. Nayenso anali ndi chikwakwa chakuthwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mngelo wina anatuluka m'Kachisi ali m'Mwamba, nakhala nacho chisenga chakuthwa nayenso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mngelo wina anatuluka mʼNyumba ya Mulungu kumwamba ndipo nayenso anali ndi chikwakwa chakunthwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mngelo wina anaturuka m'Kacisi ali m'Mwamba, nakhala nalo zenga lakuthwa nayenso.