Revelation 15:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zitatha izi, ndidaona Kumwamba Malo Opatulika a m'katikati mwa Chihema cha Umboni atatsekuka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo zitatha izi ndinaona, ndipo panatseguka pa Kachisi wa chihema cha umboni m'Mwamba:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zitatha izi, ndinaona kumwamba Nyumba ya Mulungu imene ndi Tenti ya Umboni, atatsekula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo zitatha izi ndinaona, ndipo panatseguka pa Kacisi wa cihema ca umboni m'Mwamba: