Revelation 16:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adayamba kunyoza dzina la Mulungu wa Kumwamba chifukwa cha zoŵaŵa zao ndi zilonda zao. Komabe sadatembenuke mtima ndi kuleka zochita zao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nachitira mwano Mulungu wa m'Mwamba chifukwa cha zowawa zao ndi zilonda zao; ndipo sanalapa ntchito zao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anatukwana Mulungu wakumwamba chifukwa cha maululu awo ndi zilonda zawo koma anakana kulapa pa zimene anachita.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nacitira mwano Mulungu wa m'Mwamba cifukwa ca zowawa zao ndi zironda zao; ndipo sanalapa nchito zao.