Revelation 16:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ndidamva mngelo wolamulira madzi uja akunena kuti, “Mwachita chilungamo m'mene mwaweruza motero, Inu Woyera uja, amene mulipo ndipo munalipo kale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinamva mngelo wa madziwo nanena, Muli wolungama, amene muli, nimunali, Woyera Inu, chifukwa mudaweruza kotero;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka ndinamva mngelo wolamulira madzi uja akuti, “Inu mwachita chilungamo, Inu Woyerayo, amene mulipo ndipo munalipo;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinamva mngelo wa madziwo nanena, Muli wolungama, amene muli, nimunali, Woyera Inu, cifukwa mudaweruza kotero;