Revelation 17:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mngelo uja adandiwuzanso kuti, “Madzi unaona aja amene mkazi wadama uja wakhalapo, akufanizira mitundu ya anthu, makamu a anthu, mafuko a anthu ndiponso anthu a zilankhulo zosiyanasiyana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anena ndi ine, Madziwo udawaona uko akhalako mkazi wachigololoyo ndiwo anthu, ndi makamu, ndi mitundu, ndi manenedwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka mngeloyo anati kwa ine, “Madzi amene unawaona pamene mkazi wadamayo anakhalapo ndiwo anthu ochuluka, mitundu ndi ziyankhulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anena ndi ine, Madziwo udawaona uko akhalako mkazi wacigololoyo ndiwo anthu, ndi makamu, ndi mitundu, ndi manenedwe.