Revelation 17:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mkazi unaona uja akufanizira mzinda waukulu uja wolamulira mafumu onse a pa dziko lapansi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mkaziyo unamuona, ndiye mudzi waukulu, wakuchita ufumu pa mafumu a dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkazi unamuonayo ndi mzinda waukulu umene ulamulira mafumu a dziko lapansi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mkaziyo unamuona, ndiye mudzi waukuru, wakucita ufumu pa mafumu a dziko.